
Ophunzira ku Unima akuganiziridwa kuti ali ndi Cholera ku Zomba
A zaumoyo ku Zomba ati ophunzira wa ku sukulu ya ukachenjede ya Unima wagonekedwa mchipatala ku Zomba ndipo akuganiziridwa kuti ali ndi Cholera. Malingana ndi a Arnold Mndalirs omwe amayankhulira ofesi ya za umoyo ku… ...