Ebrahim Raisi
Tsogoleri wa dziko la Iran, Ebrahim Raisi wamwalira pa ngozi ya Ndege ya mtundu wa helicopter yomwe inanyamula mtsogoleriyu ndi nduna yoona za maiko ena ya dzikolo, Hossein Amirabdollahian. Malinga ndi malipoti omwe  wailesi ya… ...
Alimi m'dziko muno awalangiza kuti azibzala mbeu zosiyanasiyana ngati njira imodzi yothana ndi vuto losowa chakudya chokwanira komaso kusintha kwa nyengo. Mkulu wa Lilongwe District Agriculture Extension Coordinating Committee (DAECC) Akunsitu Kananji ndiye anayankhula izi… ...