Mbeza
Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lakana pempho la belo la mkozi wa nyimbo Chiyanjano Mbeza yemwe anamangidwa poganizilidwa kuti wakhala akutulutsa ndi kufalitsa mauthenga onyoza mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera. Malingana ndi oweruza… ...
Kasman
Apolisi munzinda wa Lilongwe atsimikiza kuti nzika ya m’dziko la Britain ya zaka 26 yabedwa ndi anthu osadziwika pomwe imachokera ku mapemphero Lolemba masana.  Malingana ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu,… ...
Chiyanjano Mbeza
Nkozi wa nyimbo Chiyembekezo Mbeza yemwe akuganizilidwa kuti wakhala akufalitsa mauthenga opatsa mantha komanso onyoza mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera, agonanso mchitokosi kufikira Lachisanu pomwe bwalo la milandu likapeleke chigamulo pa pempho la belo. … ...