Anthu ayamba kulozerana nyumba ya malemu Goodall Gondwe
Nanga inu adzalozerana chiyani mukadzatsamaya? Ndalama osamangodya ngati kuti ndi tomato yemwe mukuopa kuti awola mukakhalitsa naye: anthu uku atutumuka ndi chinyumba cha malemu Goodall Gondwe, ndipo kuli kulozerana kwinaku akuomba m’manja kuti Phuu! Kuli… ...