![Matako](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/Lilian-Matako-235x176.jpg)
Matako apatsidwa chilango chogwira ntchito zosalipidwa
Bwalo la Senior Resident Magistrate Joshua Nkhono ku Balaka lalamula kuti a Lilian Matako komanso a Ishmael Chitete akagwire ntchito zosalipidwa m'dera lawo atapezeka olakwa pa mlandu ovulaza munthu mwadala. Awiriwa adamangidwa zitadziwika kuti adapeleka… ...