Chakwera m’busa wabodza

...anama kuti ndalama zaboma zinathandiza amalawi kuthawa Covid ku Joweni A Malawi omwe anavotera mtsogoleri Lazarus Chakwera chaka chathachi awuzidwa ndi mtsogolerIyu kuti anachalira vimadzi vamphusi chifukwa iwo sali pano kukwaniritsa lonjezano lomwe ananena. Ena… ...