Malawi24
Ophunzira wina wa zaka khumi (10) m'boma la Phalombe, wafa atagundidwa ndi njinga yamoto dzulo Lamulungu pomwe oyendetsa njingayi anakanika kuyiwongolera kamba kothamanga kwambiri. M'neneri wa polisi ya Phalombe, a Jimmy Kapanja, watsimikiza za nkhaniyi… ...
TikTok Daddy
Mnyamata amene amadziwika bwino ndi dzina loti iPhone Daddy patsamba la mchezo la TikTok, Innocent Sengimana wazaka 23, wamangidwa ndi apolisi ku Area 3 munzinda wa Lilongwe kamba kobera anthu ndalama zokwana 5 miliyoni kwacha… ...