Namadingo said this in Times Exclusive interview with Brian Banda aired on Times Television on Saturday.
"Mwayamba za ndale?" Anthu angoti kukamwa pululu pamene Dr Namadingo amene amadziwikanso bwino ndi dzina loti Doc walengeza  kuti “2030 boma” ndipo anthu akhale tcheru. Izi zadzetsa mafunso ochuluka kwa anthu amene amamutsatira bwino. Namadingo… ...
Mayendedwe akhala ovutirapo pamene mlatho wapamtsinje wa Chitete omwe uli pafupi ndi sukulu ya sekondale yoyendera ya Boma Community Day Secondary school (C.D.S.S) mumanisipalite ya Kasungu wakokoloka ndi madzi kutsatira mvula yamphamvu yomwe yagwa kuyambira… ...
Suicide
Bambo wina ku Dowa  yemwe dzina lake ndi Kelvin Songazaudzu wa zaka 47 zakubadwa wadzimangilira kudenga la nyumba yake kaamba kamavuto a m'banja. Mneneri wa apolisi m'bomali a MacPatson Msadala watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati… ...