Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno, la Malawi Electoral Commission (MEC) lati anthu omwe ali ku Israel komanso mayiko ena akunja sadzakhala nawo mwayi oponya mavoti pa zisankho za patatu zomwe zidzachitike m'mwezi wa September chaka… ...
Articles By Ben Bongololo
Apolisi ku Kasungu akusunga mchitokosi njonda ina ya zaka 35 zakubadwa kamba kopezeka ndi katundu monga wayilesi za kanema zinayi za mtundu wa plasma ndipo njondayi ikuganiziridwa kuti idachita mokuba katunduyi. Wachiwiri kwa mneneli wa… ...
Tsopano nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati kuyambira mawa pa 1 February mvula ikhala ikugwa m'dziko muno patapita pafupifupi sabata ndi masiku kopanda mvula maka m'madera am'chigawo chapakati komanso kum'mwera kwa dziko lino.… ...
Sukulu ya ukachenjede ya Luanar yapereka zilango kwa ophunzira okwana 19 kamba kopezeka olakwa pa mlandu owonera mayeso ndipo atatu mwa ophunzirawa awachotsa sukulu. Ophunzira pamene khumi ndi anayi ayimitsidwa sukulu kwa zaka ziwili, ena… ...
Dziko la Japan lapereka ndalama zoposa 1.99 biliyoni kwacha kudziko la Malawi kudzera ku bungwe la UNICEF kuti zithandizire kuthana ndi ena mwamavuto omwe alipo m'madera ena omwe anakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy. Malinga ndi… ...
M'modzi mwa akatswiri omwe amayankhulapo pa nkhani za mdziko muno, a Lyford Chadza, ayamikira boma kaamba kothetsa mlandu wa anthu atatu omwe adanjatidwa kamba kosokoneza galimoto zapa m'dipiti ponena kuti izi zidakaononga ubale wabwino pakati… ...
Boma kudzera mwa nduna yoona zamagetsi mdziko muno a Ibrahim matola, lalonjeza kuti lithandiza nyamata uja wakonza magetsi oyendera madzi ndi mpweya ku Dowa kufikira masomphenya ake oyika magetsi pa sukulu ya Kongwe 2 komanso… ...
Makosana awili ku Lilongwe athilidwa zingwe ndi apolisi kamba kowaganizira kuti akhala akubera anthu ponamizira kuti ndi ochita bizimezi yoyendetsa galimoto zonyamula anthu. Nkhani yonse ikuti makosana awiliwa omwe mayina awo ndi a Alick Kazembe… ...
Ogwira ntchito anayi apa kampani yogulitsa zipangizo za ulimi ya Export Trading Group (ETG) awanjata ndikuwaponya mchitokosi cha apolisi ku Dowa kamba kowaganizira kuti adakwangwanula m'matumba afetereza pa kampanipo. Anthu anayi oganizilidwawa ndi a Sigele… ...
Boma lalengeza kuti lathetsa mlandu wa anthu atatu omwe anawanjata kamba kosokoneza galimoto zapa m'dipiti wa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pomwe ankakakwera ndege ku Chileka mu mzinda wa Blantyre. Omwe amazengedwa mulanduwu… ...
Akathyali atatu akhwidzingidwa ndi apolisi ku Lilongwe kaamba kowaganizira kuti adayendetsa champeni (kuba) lamya za m'manja za anafedwa pamaliro dzulo m'mudzi wa Kamganga kwa mfumu yaikulu Mavwere m'boma la Mchinji. Nkhani yonse ikuti akathyali atatuwa… ...
Poona kuti ophunzira ambili mdziko muno akulephera kupeza nawo mwayi ochita maphunziro msukulu za ukachenjede m'dziko lino kaamba ka chingerezi (English), yemwe ndi katswiri pankhani za maphunziro wapempha boma kuti lichotse chingerezi ngati phunziro limodzi… ...
Mfumu ina yazaka 40 ku Lilongwe yalamulidwa kukaseweza jere kwa zaka 20 itapezeka yolakwa pa mlandu oti idagwilira mwana wazaka 13 m'munda wachimanga pamene mwanayo amkatchola nkhwani atatumidwa ndi amake. Malingana ndi mneneri wa apolisi… ...
Bungwe la National Advocacy Platform ladzudzula khalidwe lotchingira ndi kugenda galimoto za pamdipiti wamtsogoleri wa dziko lino ponena kuti simoyo wabwino ndipo onse okhudzidwa pa mchitidwewu akuyenera kuzengedwa Malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa ndipo… ...
Boma latsindika ku mtundu wa a Malawi kuti limanga mabwalo amasewero a matimu a Mighty Mukuru Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets mu mzinda wa Blantyre. Nduna yoona za achinyamata ndi masewero mdziko muno a… ...