Anthu awili afa ndipo ena avulala pangozi yagalimoto yomwe yachitika lero pamudzi wa Machinga m'boma la Dowa mu nsewu wa Salima-Lilongwe pamene galimoto yomwe anakwera inalephera kukwera chitunda zomwe zinapangitsa kuti ibwelele m'mbuyo mpaka kukagwera… ...