Simplex Chithyola Banda
Mpungwepungwe unakula m'nyumba ya malamulo pamene mbali ya boma yavomereza lamulo kuti ulimi wachamba udzilimidwa m'dziko muno. Izi zinadzetsa mpungwepungwe kunyumbayi pamene aphungu achipani chotsutsa cha Democratic Progressive Party (DPP) anati sakugwirizana ndi lamuloli. Izi… ...
Lazarus Chakwer on 23 March 2024 when he declared a state of national disaster in Malawi
M'modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pazochitika m'dziko muno Lyford Chadza wapempha alangizi a mtsogoleri wa dziko lino kuti adzimuwunikira mtsogoleriyu mwatchutchutchu ponena kuti a Chakwera achedwa kulengeza kuti m'dziko muno muli njala. A Chadza ati… ...
Bwalo la milandu ku Lilongwe lalamula a Arafat Goman kukakhala kundende kwa zaka 63 pa mlandu wakupha a Cecilia Lucy Kadzamira azaka 82 amene adali mchemwali wa a Tamandani Kadzamira, mthandizi wa mtsogoleri wakale wadziko… ...