Prophet Habakuk
Patangodutsa sabata imodzi pomwe Prophet Shepherd Bushiri adapeleka ndalama zokwana 6 miliyoni kwacha kwa 'M'neneri' Habakkuk kutsatira pempho lomwe adapereka, lero Habakkuk wapemphanso thandizo lina kwa m'neneli Bushiri. Mneneri Habakuk ati akufuna thandizo loti amangire… ...
Wanderers
Ayi ndithu lero mu Tnm Super League zavutirapo ndithu pamene imodzi yokha ndiyo yaluza pamene ena anayi afanana mphamvu pakutha kwa masewero lero pa 11 May 2024. Mighty Mukuru Wanderers yamwa mkaka wa ngambwingambwi pomwe… ...
Kunali kumwemwetera chakumasanaku ku Dedza pamene timu ya Dedza Dynamos yatembenuza chikwangwani nkukhala Premier Bet Dynamos kutsatira mgwilizano omwe timuyi yasayinira ndi kampani ya Premier Bet wandalama zokwana 100 miliyoni kwacha. Kampaniyi yati iziperekanso ndalama… ...
M'nyamata wina amene wakhala akunamizira kuti ndi ophunzira pasukulu ya Ukachenjede ya Mzuzu ali mu uluru osaneneka kutsatira kumenyedwa ndi ophunzira pasukukuyi pomuganizira kuti anaba mafoni awiri awophunzira ena. Amon Chimalawalana, yemwe watiuza nkhaniyi, wati… ...
Kunali mkoke mkoke lero mu Tnm Super League pamene anyamata amakudzulana nthenga, kugwalulana zibwano, kuchotsana chimbenene. Uyu ndi tsatanetsane wamomwe lero masewero athera. Mighty Wanderers yalepherana ndi timu ya Bangwe All Stars, ndipo masewero athera… ...
HIV law has remained unknown to many since its introduction in 2018. The National AIDS Commission (NAC) is raising the alarm that a large part of the population is unaware of the HIV and AIDS… ...