Gabadinho Mhango
… Chifukwa walabvulira mzake  Wadyanso wani Gabadinho Mhango mu dziko la South Africa. Ambiri akukamba za iye. Koma m'malo momuyamikila kuti ali ndi luso logometsa mafuko pokankha chikopa, anthu akuti khalidwe la Gaba ndi lonunkha… ...
prostitution malawi
Nawo ndi a Malawi ndipo atopa ndi zotsalidwa. Tsopano akupempha kuti boma liwathandize kuti nawo azimva kuti ndi mzika za dziko lino. Amayi oyendayenda auza boma kuti lisiye kuwayang’anila pansi ndi kuwathandiza kuti nawo azikhala… ...
Carlsberg Cup
Awatibulanso. Kachikena awatsambitsa madzi a matope. Ku Bingu anapita akusangalala kuja, Manoma atuluka ndi nkhope zozyolika akulila mayomayo. Pa masewero amene anakodola khamu, maule lero aliritsa nyerere kachikena atazitsomphola chikho cha Carlsberg. Anali masewero oyamba… ...
Uladi Mussa
...JB has no mandate over PP, says Uladi Mussa Things have fallen apart in People's Party where Uladi Mussa, the party's acting president, has said he no longer recognises Joyce Banda as PP's president. Change… ...
A Roman Catholic priest serving Balaka Parish was found dead on Wednesday. According to the Catholic Secretariat of the Episcopal Conference of Malawi (ECM), Reverend Father Callisto Baluwa of the Society of Montfort Missionaries was… ...