Mahule akufuna chithandizo cha boma

Advertisement
prostitution malawi

Nawo ndi a Malawi ndipo atopa ndi zotsalidwa.

Tsopano akupempha kuti boma liwathandize kuti nawo azimva kuti ndi mzika za dziko lino.

Amayi oyendayenda auza boma kuti lisiye kuwayang’anila pansi ndi kuwathandiza kuti nawo azikhala ndi moyo osangalala mu dziko muno.

sex-workers-new
Amayi oyendayenda auza boma kuti lisiye kuwayang’anila pansi.

Iwo ananena izi mu boma la Ntcheu pamane anakumana ndi akuluakulu a bungwe la National AIDS Commission.

“Akakhala ogwila ntchito mu zipatala ndiye amatitenga ngati sife a Malawi ndi komwe. Akangozindikila kuti ndiwe mzimayi oyendayenda ndiye amatha olo kukana kukupatsa chithandizo. Ena ndiye amakuuza kuti agone nawe kuti akuthandize,” anamang’ala chotelo mmodzi mwa iwo.

Amayiwo anapempha kuti boma liwathandize ndi maphunziro okhudzana ndi ufulu wawo, ndi kuwapatsa upangili odziwa njira zothanilana ndi akuluakulu a boma amene amafuna kutengelapo mwayi oti iwo ndi mahule ndiye awachitile nkhanza.

 

 

Advertisement

146 Comments

 1. Kkk amaasala ndani,??mwagoganiza nokha , Uhule unalipo kuyambila kalekale yesu asanatifele,,,mwini olenga azathesa yekha ndipo sikale popano koditu umbuli siwabwino chilichose kumagoti boma utsilu eti , pali ambili anasiya okha ndipo pano ndizika zobalilika coz mulungu anayendela mwapadela

 2. kkkkkkkkkkkkkkkkkk Chithandizo chachani apa??ngati boma likufuna kuthandiza, lithandize anthu omwe ali mu prison not mahule.

 3. Amenewo anena zoona ayenera kuthandi zidwa zikakhala ntchito zawozo azaweruza ndi mwini mulungu Iwo so ndi dzika zamalawi palibe so kuwanyoza ai

 4. Musayiware ambiri mwa iwo amasuta even fodya opanda shade uja amathanso kubandika ndiye osamadabwa akamapanga zokhala ngati asali normal

 5. Ndizachisoni pamene ziko likupita kumapeto ndichifukwa chiyani asikana okongola ngatiinu kusamkha kukhala mahule ganizani bwino ambuye akuyendeleni

 6. Akayamba kulandila ndalama ndy ambili akhala mahuletu …Nanga kusalidwako akumawasalayo ndindani? Mwina adakanena nkhani za nkhanzatu chifukwa ena amawapangila nkhanza…

 7. Zopepela!!! kodi boma lamalawi ndilomwe linawalemba ntchito yauhule? Mmalo moti azit Mulungu awathandize kut chiwanda chomwe alinacho chichoke.Ayambe kuyenda mchiyelo chake.Ndie ali busy kumanena zinthu zopanda pake ngat anapanga mgwilizano ndiboma!! ndikunenesa kut uhule siuzawalemekezetsa pamatso pao forever untill Jesus com

 8. Zopepela!!! kodi boma lamalawi ndilomwe linawalemba ntchito yauhule? Mmalo moti azit Mulungu awathandize kut chiwanda chomwe alinacho chichoke.Ayambe kuyenda mchiyelo chake.Ndie ali busy kumanena zinthu zopanda pake ngat anapanga mgwilizano ndiboma!! ndikunenesa kut uhule siuzawalemekezetsa pamatso pao forever untill Jesus com

 9. Their concerns should be heard. Its not a crime to be sex worker in Malawi. Azibambo, ndani sanapanepo hule muno? Ngat ali oipa why do we hook them??

  1. then they shuold consult their customers who comes to purchase their cimmodity not Govt at large.its not a crime to be hule but thumba latambe amamasula ndi tambe yemweyo.apeze mahule anzawo achimuna awauze zimenezo.za ziiii

 10. Most of the comments show misunderstanding of the issue. The prostitutes are not asking for a wage or salary from government. They are asking the government to protect them and their trade and also sensitise the Malawi population that they, the prostitutes, should also be treated like any other respectable citizen of this country without segregation and without being looked down upon as the case is now. My view, however, is that theirs is not a respectable profession and should not ask government to help them to gain respect. They just need to quit their trade.

 11. Had They Known ,BINGO had an idea that they should hav a uniform for recognation but they said its harrasment now its too late kk pitani muzikalima

 12. panyopanu anakutumani uchisiluo ndibomalo nengati mwatopa kugonedwa bwanji osakapuma mumakwanu bwanji zopusa basi chithandizocho bwanji osapasa ana amasi

 13. bwanji, malonda omwe amachita sakuyenda bwino pamnsika? azilandila ngati ndani? amawatuma kuti azikaima m’iseu ndani? ndi zomwe mtima wao, unasankha, kodi boma ili, anthu akumalionerera choncho bwanji, posachedwapa ena akhala akuchita m’bindikilo kwa masiku ochuluka akuti boma liwapse ndalama chikhalilenicho anali achipani malo mopita kuchipaniko akulimbana boma, mahulenso naonso ayamba kenako amaskini kenako aliyense aziti tili mziko muno nafenso tizilandila, ai mahule idyani thukuta lanu

 14. kkkkkkkkk koma kumalawi kwavuta bas ndimahule amene azilipidwa ndi boma ngati amatombesa ulele zachamba!! .uhule ndi tchimo ndipo tchimo limazuza .Ngati sakuyenda malonda sivuto laboma coz palibe anawatuma.

 15. zodabwisa izi gyz itanani bushuli apemphelele malawi mahule akufuna chithandizo pomwe amasiye akusowa xool fees antchito zaboma akudandaula ndi tindalama tomwe amapasidwa,Akangopeleka ma gyz tilumikizane tiyambise chisoknezo unless abomawo azanene kuti kuli bungwe lamahule,akatelo ife oitanila mabasi nafe tipemphe chithandizo kuboma.akapeleka boma nde ndi mbuzi.ayese kupeleka ativa ife anthu akumpoto timadanandi zopusa

 16. haha they av done what tu recieve salary….. kungodzuka basi claiming money for nothing …. stupidness ……. its their business beneficial to this country’s economy…….. we are misusing human rights… all bullshit

 17. Sakumapereka nsonkho pa business yawoyo. Ngati akufuna thandizo laboma, tiwerengesani kuti akakumana ndi mamuna, azipereka nsonkho per round

 18. They are human beings yes but this their job is too shameful and God blaspheming one. We understand the poverty in our country Malawi komano zafika pena pake. We ca see that ena sakupangira uhule kaamba ka umphawi ndi ana a ma bwana ena makolo onse alipo ndipo amazipezera but their duaghters are attacked by the spirit of fornication. We have alot in Liwonde ku block 6, mot kukada pa Idols ndo woza woza, ambiri sabera amuna ayi koma azibambo akunyoza ma anja awo kaamba koti akagona ndi mahulewo amaona ngati afika kumwamba.
  How shameful it is in Mozambique, go Quelimane, they are thothotho kumeneko, go to Cuamba and Lichinga abale zamanyazi, if have ever reached Nampula muzalira and you will hid yourself as a Malawian, atsikana ali pa res thouse bar yotchedwa Axinene (Eni thaka kapena kuti eni wake ) Mahule ndipo afatsa mpaka adzadza ma rest house atatu wozungulira pamenepo and akuitanitsa mbava pajatu mbava ndi hule zimamvana.
  Wina anaphedwa mu room two months ago makolo ake anabwera kuchokera ku Malawi kuzaika thupi la mwana wawoa imigratio ku Moz anazawagwira nkuwatumiza ku Mandimba koma anakagona ku Mangoch mawa lake nkubwelera, uku akamachoka amauza makolo ndi abale kuti akukachita busines ku Mozambique, boma la Malawi lichitepo kanthu ife zikutichititsa manyazi, amatukwana ukakana kugona nawo.
  Malawi linali dziko labwio and Africa could appreciate the culture we had and the respect and loyalty of our women but today anthu mayiko wotizungulira yamaba kuwakayikira akazi aku Malawi, eish, go to South Africa akulandira ma 10 Rands a

  1. Inde mpaka akumafalitsa kuti Ku Mozambique ndiko kuli yothentha. Amakhimbitsa kulandira ma duzentos (2000 meticais, how shamefuloooh!!!!!!!

 19. Boma lasowazo chitanazo ndalamazo bola kuwonjera malipilo anthu amene akugwira ntchito zenizeni ngati mwatopa ndia zimuna kalimeni agalu inu

 20. something that can be bought or sold is an ”object” trust me it can be bargaained so noway should they expect dignity yet they are selling the very thing that they are asking dignity for.

  1. Seriously.? Arent they selling in reality? How do one dignify a bargaining object? Bring up your argument. I hate the activity not the people.

 21. Can Prostitutes Nd Acctac Frm De Govt? Sports Or Wat? De Govt Doesn’t Allow Prostitution At All.So Can It Acct Ppo Wo Operate Illegal Business? F It Z Going 2 Help Dem, Obviously De Govt Itself Recognises Prostitution.

 22. Bomalo poti atsogoleri ake ndi mbudzi zawanthu muona akupereka thandizolo chomwe akudziwa agalu amenewa sikuletsa anthu anchere kukasaka Ku theba koma kuvomereza thandizo la mahule

 23. Ngati mwatopa ndi uhule basi mudzikangolima kumudzi .Bomalo nalo lasowa chochita Aaaasa Mbudzi za anthu ndani anakutumani kuti mudzikapanga uhule iya

 24. Ndi pomwe mungadziwe kuti dziko lili manja asatana kale zinali zochitisa manyazi kupanga uhule pano ndi part of life

 25. Mahule akugwira ntchito yotamandika kuposa anthu omwe amazitcha opemphera ndipo mufune musafune mulungu akayamba kulanga anthu opempheranu kenako mahule

 26. Do they pay tax? I am a tax payer but I am hustling on my on without any government help. Then someone who don’t contribute taxes is asking government help to up hule business. They must pay tax first otherwise if government give them money then I stop paying tax.

 27. Boma limakana chamba chomwe chimabweretsa ndalama mdziko ndiye livomere uhule lipindula chyani? Mahule amathandiza chani pa chitukuko cha dziko?

 28. Ana osamvera amachitisa manyazi makolo awo… Akanakhala kuti ankawamvera makolo awo bwez pano sakudadaula ndi zopusazi.. Apite akawapepese makolo awo ndikuyamba moyo wina. Kapena akufuna fees? Hahahaaa, atenge ngongole akaphunzile basi kkkkk

 29. These ” lesbians” must not listened to their grievances. What we need to them is only to ” banish them” from our land coz they are devils/ satans/ evils.

 30. Zopusa basiiii…. Azanu azimayi akuthamanga pa town kumagulisa mandasi Ka zitumbuwa koma umoyo unka kupta chisogolo mxng kochepako akukwanirisa kulipirira mafana awo xool fiz

  1. Boma liwathandize pazomwe Iwo akufuna kuti liwathandizee nawo ndi anthu oti anaponyaa vote so let government help them on what they seek from them

 31. Kkkkkkkl Dziko lamalawi lili pamoto ndithu..mahule akufuna azilandiraso ndalama zaboma pakutha pamwezi kkkkkkkk komanso ngat watopa nawo uhulewo azitha kumalandira ndalama za peshoni kkkkkk..Dzina loti hule ili muzalikanatu inu patsiku likubweralo muzizachita kuyang’anira kumbali wina atakukumbitsani kut paja munali ahuletu aunt muzakana ndithu kkkkkkkkkk

  1. Ndipo inu adzachita kuziiwala pa tsikuli! koma yesu ananeneratu kut azakana onse omwe samadziwa! wakumva amve!

 32. atathandzen akugwira mchito yotamandka athuwa mpaka kwa amuna osowa,ankhope zopindka ngat mjwera yokakamra mu chikombolo ,mbava,amwendo yopotoka ngat apanra ng’oma

Comments are closed.