Wakalamba wafuna. Mstogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika amene akhale ndi zaka 81 pofika 2019 ati iwo ndi kamnyamata kachisodzela ndipo azapikisana nawo pa chisankho mu 2019. A Mutharika anena izi mu mzinda wa… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
A cyberwar has ensued between Malawians and Zambians over comments that the former made on a viral photo that shows the Mayor of the Capital City of Zambia, Lusaka, taking a nap at a public… ...
Inu amene muli pafupi ndi Mtsogoleri otsutsa a Lazarus Chakwera, ati muchite machawi kuwamanga zingwe ndi kumapita nawo ku chipatala cha anthu a misala ku Zomba. Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika anena kuti… ...
Amwela chikho chimodzi tsopano pa uwiri wawo, oyimba Phungu Joseph Nkasa ndi munthu wa Mulungu Shepherd Bushiri. Pamene oyimba Joseph Nkasa watulutsa nyimbo yotonza chipani chotsutsa cha Kongeresi uku akutamandila chipani cholamula cha DPP, naye… ...
Fourteen young Malawians have left the country for South Africa where they are expected to obtain skills and experience in leadership in their various fields. The fourteen will participate in a month long YALI RLC… ...
Lawaluma lamulo ndipo lawasiyila chilema chachikulu chokuti ngakhale a chipatala sangathe kukonza. Ndipo inu nonse okonda kuchitila nkhanza ena, bisalani patali chifukwa mawa mutha kukhala inu. Amayi atatu a ku Lilongwe amene anagwila mmayi mzawo… ...
Si zampira ayi. Apa zikungokhala ngati anthu ake ndi agalu achiwewe chenicheni oti akufunika kuswa ndi miyala. Anthu ena ochemelela timu ya mpira ya Bullets akuononga masewelo a mpira kamba ka khalidwe lawo lokonda ziwawa.… ...
…feared Malawi Police presence in a ‘foreign land’ Two districts are slated to announce their secession from mainland Malawi today, proponents for this move have confirmed. According to the Peoples Land Organisation (PLO) as led… ...
In the face of serious electricity problems, Malawi President Peter Mutharika has ambushed the Electricity Generation Company (Malawi) Limited (EGENCO) management in Blantyre. The President arrived at EGENCO offices at Umoyo House in Blantyre as… ...
Inu amene mukumadzuka usiku ndi kumakolezera moto pa nkhani zopopa magazi, samalani chifukwa Apolisi ayamba kunjata anthu a mkhalidwe onunkhawu. Mkulu wina wa mu boma la Zomba walamulidwa kukakhala ku ndende kwa miyezi itatu chifukwa… ...
Salima South Legislator Uladi Mussa has insisted that he is still the party’s acting president and vice-president. The politician has claimed that the party has not told him that he was fired hence he is… ...
Amene amayesa kuti chipani cholamula cha DPP chatha ndi kufelatu basi kamba koti chathibulidwa ka ‘5 kwa 1’ ndi chipani chotsutsa cha Kongeresi, ati aganizenso kawiri. Malinga ndi mneneri wa boma a Nicholas Dausi amene… ...
Chimanga chonse chija chinayi wajomphapo Tambala wakuda, ndipo ngati a chipani cholamula amayesa kuti a Malawi adakali mtulo tsopano adziwa dziko lidasintha. Chipani cholamula cha DPP chaonetsedwa mbwadza, kapena kuti mbonaona, pa chisankho chapadela chomwe… ...
Ena sadzawaona ndi komwe chifukwa azakhala atatsogola kale. Ati nkhani ya kuvuta kwa Magetsi tidakali nayo mpaka a Peter Mutharika kutula pansi udindo. Malinga ndi a bungwe lopanga za Magetsi la EGENCO, mavuto a Magetsi… ...
A Mother's Day announcement from President Peter Mutharika carried on Malawi Broadcasting Corporation (MBC) has gone viral on social media following an error. A picture showing the announcement that said "Happy Mother's Day 'massage from… ...