“Kuthanakuthana pa ndale” – Ken Msonda waopsyeza DPP kuti imumva kunyung’unya
A Ken Msonda omwe ndi m'modzi mwa mamulumuzana omwe awonetsedwa nsana wa njira mchipani cha DPP, akuti chipanichi chaputa mavu nkhomora ndipo waopsyeza kuti chipanichi chiyembekezere kukha madzi ponena kuti pakadali pano wakufa pa ndale… ...