Malawi Police

Kachama sapepesa

Mkulu wa Malawi Police, bambo Lexten Kachama wamenyetsa nkhwangwa pamwala kuti iye, ngati yemwe anakhalapo pa udindowu a Peter Mukhitho, sapepesa kwa Jessie Kabwila. A Kabwila, omwe ndi phungu wa chipani cha Kongelesi anamangidwa pamodzi… ...