Ine ndiye Mose ine – watero Timothy Mtambo
Mudziwitseni Phungu Joseph Nkasa kuti analakwitsa. Mose wa lero ati sanali Mutharika, koma ndi a Timothy Mtambo. Atero eniake pomwe anapangitsa msonkhano wa atolankhani lero pofuna kukumbutsa kuti akadalipo. A Mtambo amene adachita chete pomwe… ...