
Khansala wa Ntiya Ward mu mzinda wa Zomba amulumbiritsa
Khansala Maxwell Finiyasi wa Ntiya Ward mu mzinda wa Zomba tsopano amulumbiritsa pankumano wa khonsolo yonse omwe udachitika Lolemba. Mlembi wa ku High Court ku Zomba Hellen Kachala ndiyemwe walumburitsa Khansala Maxwell Finiyasi. Khansala Finiyasi… ...