water tap
Ngati simufa ndi njala, ndiye mwina ludzu kapena kolera zitha kukuphani. A bungwe la Blantyre Water Board alengeza kuti madzi awo akwera mtengo. Mu chikalata chimene bungweli latulutsa, a boma tsopano awapatsa chilolezo choti madzi… ...