
Mayi wamangidwa kamba kogwilirira mwana wazaka 16
Mayi wazaka 38 yemwe dzina lake ndi Takondwa Banda ali m’manja mwa a polisi ku Kasungu kogwirira mwana wammuna wazaka 16 ndi kumupatsila matenda opatsilana pogonana. Mneneri wa polisi ya Kasungu Joseph Kachikho wati izi… ...