Amangidwa chifukwa chofuna kugulitsa mimba ku Nkhotakota
A Polisi m’boma la Nkhotakota amanga a Frank Malaki a zaka 23 ndi mkazi wawo Enita Joseph chifukwa chofuna kugulitsa mimba pa mtengo wa K200,000. Awiriwa amafuna kugulitsa mimba ya a Joseph kwa munthu wina… ...