Mutharika asambwaza Chakwera: Thana kaye ndi mavuto a mu Kongeresi kenako undilangize ine
Zimene analankhula mtsogoleri wa chipani cha Kongeresi, a Lazarus Chakwera, pa msonkhano ku Dedza kutha kwa sabata latha zawapezetsa mavuto pamene mtsogoleri wa dziko lino amene naye ali mtsogoleri wa chipani cha DPP, a Peter… ...