Yalakwa ku Kongiresi: A Chakwera achotsa anthu mu chipani, aimitsa a Kabwila ndim’khalakale a Njobvuyalema

Advertisement
Jessie Kabwila
Mikangano ya mu chipani chachikulu chotsutsa m’dzikomuno cha Kongiresi yafika pamponda chimera ndikuonekela poyera tsopano.

Patapita nthawi yaitali akuluakulu a chipanichi akukanaso kuti mulimavuto mu chipanichawo komanditianthutingapochabetolipidwa kuti tiyambitsempungwepungwe, dzulozinadziwika kuti mu chipanichi muli mavuto a zaoneni.

Pa msonkhano wa atolankhani omwe unachitika dzulo, mtsogoleri wachipanichi a Lazarus Chakwera anavomela kuti mulimavuto mu chipanichi.

“Mulimavutoaakulu mu chipanichathu, mpakaenaamafunakuotcha ma ofesiathu. Anthu a mu chipanichathuchomwekufunakuotcha ma ofesiathu,” anadandaula a Chakwera.

Jessie Kabwila
Kabwila waimitsidwa pa mpando.

Kwa nthawiyoyamba, a Chakwera anavomela kuti palikuukilanapakatipawondipooyambitsasi a zipanizinakomaeniake.

Pa msonkhano omwewo, a Chakwera analengeza kuti achotsa mu chipani anthu ena kuphatikizapo phungu wadera la pakati mu boma la Salima, a Felix Jumbe, amene anapikitsana nawo pa mpando wamtsogoleri wachipanichi.

A Chakweraanalengezanso kuti chipani cha Kongeresichachotsa MayiChatinkhaChidzanja Nkhoma amene kwa nthawi yaitali akhala akuwadzudzula.

Anaonjezelapokulengeza kuti chipanichi chaimitsa pa udindo  mphunzitsi wakale waku sukuluya ukachenjede amene analimneneri wa chipanichi, Mayi Jessie Kabwila kuphatikizapo a Joseph Njoubvuyalema. Awiriwa akuganizilidwa kuti anatuma zigawenga kukaotcha likulu la chipanichiku Lilongwe. Chodabwitsa ndicha kuti galimotoya  Mayi Kabwila idatenthedwa moto mu ngozi yosaoneka bwino bwino ndipo eni ake anati anachitidwa chipongwe ndi anthu.

Koma pothililapo ndemanga pakuchotsedwa kwawo, Mayi Chidzanja Nkhoma anaseka .

“Inetu MCP sindinachite kulowa ngati a Chakwera, ndinabadwilamommo. Iye ndindani kuti akandichotse?” anadabwammotero a Chidzanja Nkhoma.

Advertisement

3 Comments

  1. THOSE AXED SHOULD NOT COME BACK. IF THEY COME BACK, THEY SHOULD FORM THEIR OWN MCP, WHICH SHOULD BE CALLED MCPJUMBE, THE OLD MURDEROUS MCP. AS FOR US, FOLLOWERS, WE ARE FOR CHAKWERA MCP. NGATI AKUFUNA MAUDINDO, APATSENI PAKUTI AKUTI CHIPANICHI NDI CHA MAKOLO AWO. MCP IS NOT FOR THE CENTRAL REGION ONLY.

Comments are closed.