Yambani kulongedza ife tidzakonze zinthu, Kabambe wauza a Chakwera
M'modzi wa anthu omwe akufuna utsogoleri ku chipani cha DPP a Dalitso Kabambe awuza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti ayambe kulongedza popeza kuthekera kokonza zinthu alibe. Malingana ndi a Kabambe omwe anakhalapo… ...