A Msonda amafuna kulanda katundu ku DHL
M’modzi wa akuluakulu a chipani cha DPP a Ken Msonda lero amafuna kukalanda katundu ku ofesi ya DHL ku Lilongwe ponena kuti kampaniyo inakanika kutumiza lita limodzi la mankhwala azitsamba obwezeretsera chitetezo mthupi omwe a… ...