Chakumwa nacho Chakwera

Kampani yofulula mowa ya Castel yalengeza kuti mitengo ya zakumwa zawo zoiwalitsa mavuto amene dziko lino likukumana nawo azikweza. Ati kuyambila mawa, mowa ukhala okwelelako mtengo. Malinga ndi chikalata chomwe kampaniyi yatulutsa, mitengo ya mowa… ...