University of Livingstonia
Sukulu ya ukachenjede ya University of Livingstonia (Ekwenden Campus) yalengeza kuti yakweza sukulu fizi ndipo izi zikhudza ophunzira amene akudzayamba kumene komanso omwe omwe akupitiliza maphunzilo awo pasukuluyi. Malingana ndi chikalata chomwe sukuluyi yatulutsa, kusinthaku… ...