Peter Mutharika

A Mutharika athawa

Abanduka dzulo kulisiya dziko liri pamoto. Pamene aphunzitsi a ku Primary komanso ena a ku Secondary anyanyala ntchito, mtsogoleri wa dziko Peter Mutharika lino wathawanso kumapita kunja. A Mutharika anyamuka ku Malawi dzulo masana ati kupita… ...