
Kwakwana-kwakwana tiyeni tipatsane ulemu – Chisale
Mkulu wa achinyamata mu chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Norman Chisale achenjeza anthu ena omwe akulondalonda iwo komanso otsatira chipani cha DPP kuti tsiku lina adzabwezera, ndipo apolisi omwe adawombera m'modzi wa ma membala… ...