Odwala khate adandaula za kusalidwa
A Thomas Damiyano a m'mudzi mwa Kazembe Mfumu yaikulu Kachindamoto M'boma la Dedza ati chiwapezereni ndi nthenda ya Khate chaka chatha moyo wawo sunasinthe kwenikweni chifukwa akukwanitsabe kugwira ntchito zomwe zimawapezetsa ndalama pa moyo wawo… ...