Soldier Lucius Banda Saulos Klaus Chilima
The Movement that is supposedly led by Malawi Vice President Saulos Chilima who has not yet communicated in person his political plans keeps gathering momentum. Now, musician Lucius Banda has joined the team. Days after… ...
Saulos Chilima Richard Msowoya
The United Transformation Movement ( UTM) has gotten a huge boost ahead of the 2019 elections with top politicians announcing their joining of the movement. Speaker of Parliament, Richard Msowoya has joined the movement, reports… ...
pp
Ehede! Mwawakumbukila aja ankalandira za Lutepo aja uku akuzitukumula. Aja anali ndi galimoto kholophethe ali mu boma aja. Tsopano akuti maluzi awasasantha. Mneneri wa chipani cha PP a Noah Chimpeni wati chipanichi chilibe ndalama zoti… ...
Peter Mutharika
Ikuvuta kuijama iyiyi. Akanakhala a Chilima mwina akanatimasula kuti paja akakhala pa mkhate si umo avutila kupha. A Malawi ochuluka ati Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika atule pansi udindo wawo ndipo afufuzidwe. Pa… ...
Zida zija anasula a Mutharika kuti anyenye a Chilima ndi owatsatila tsopano zilibe ntchito. Kutukwana konse amachita Mayi Kaliati nako kulibe fungo. Tsogolo silikuoneka bwinobwino. A Chilima ati afotokoza bwino lino. Atakola chidwi cha a… ...
Peter Mutharika
Inu owelenga Baibulo, mwaikumbukila nkhani ya bulu anakwelapo Yesu ija akukalowa mu Yerusalemu? Ngati mwayiwala, dikilani tikukumbutseni. Paja Yesu anatuma ophunzila kuti apite mmudzi, ndipo akapezamo bulu ndipo akamumasule ndi kumupititsa kwa iye. Aliyense akafunsa,… ...