
Ndi lerotu neba pa Balaka. Kukakhala ku banja la maule, usikuwu anagona tulo tofa nato podziwa kuti malo awo mu ma semi alipo kale. Palibe olanda. Nyerere kapena kuti manoma ali ndi ntchito yaikulu lero… ...