Peter Mutharika
Ati za Chilima muiwale. Ngati aimile ndiye mwina chipani china basi koma kuja ku DPP, palibe amene akufuna a Mutharika achoke. Anthu ali nganganga pambuyo pa a Mutharika. Komiti yaikulu ya chipani cholamula cha DPP… ...