Malaulo: Mfumu yapereka pathupi kwa mwana wazaka 16
Zina ukamva ngati kumaloto ndithu. Apolisi m'boma la Kasungu amanga mfumu Mwimira yazaka 52 kamba kogwilira mdzukulu wake wazaka 16 ndikumpatsanso pathupi. Malingana ndi mneneri wa apolisi m'bomali a Joseph Kachikho, makolo amwanayu anadabwa kumuona mwanayu… ...