Imwani Kombucha mosalekeza mulibe bibida, simudzaledzera – atelo opangawo
Fisi anakana nsatsi: kampani yopanga zakudya ndi zakumwa ya Nutricom Foods and Beverages, yakana mwantu wagalu kuti chakumwa cha Kombucha chomwe imapanga muli mphamvu yoledzeretsa. Nkhaniyi ikudza pomwe kampaniyi ikudzudzulidwa kuti chakumwa chawo cha Kombucha… ...