
Ofesi ya zaumoyo ku Zomba yayamba kupereka mankhwala a Likodzo
Ofesi yadza Umoyo Boma la Zomba yati yayamba kupereka mankhwala alikodzo komanso mankhwala a njoka zammimba kwa ana omwe ndi oyambira zaka zisanu (5) zakubwadwa kulekedza zaka khumi ndi zisanu zakubwadwa (15). Wofalitsa nkhani ku… ...