Zitsulo kunolana: A Muluzi awuza a Mutharika kuti athetse mpungwepungwe mu DPP
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi alangiza mtsogoleri wakale a Peter Mutharika omweso ndi mtsogoleri wa chipani cha DPP kuti ayese kuthetsa kusagwirizana komwe kulipo mchipanichi. A Muluzi ayankhula izi Lamulungu pa 10… ...