A Muluzi asusula chilonda

Ochita ziwonesero ndikusakondwa kwa zotsatira za chisankho cha pa 21 May, awonetsa mkwiyo wawo kwa mtsogoleri wakale wa dziko la Malawi a Bakili Muluzi powakumbutsa za mlandu wawo wakatangale. Padziwonetsero zomwe zidachitika lachinayi m’dziko muno,… ...