Kazembe wa dziko la Amerika m'dziko muno, David Young, watsanzika potsatira kutha kwa nthawi yake ya ukazembe. Mu chikalata chomwe ofesi ya ukazembe wa dziko la Ameleka yatulutsa chati a David akhala pa udindo wa… ...
Bungwe la Evangelical Association of Malawi (EAM) lapempha anthu onse dziko muno kuti pakhale mapemphero apaderadera opemphelera mvula kamba ka ng'amba yomwe yakhudza m'dera ambiri m'dziko muno. Chikalata chomwe wasainira ndi mlembi wamkulu m'bungweli, M'busa… ...