Police
Nthambi ya apolisi dziko muno yachotsa ntchito apolisi awiri amene amagwira ntchito m'boma la Thyolo chifukwa cha kulephera kusunga mwambo komaso kujomba ku ntchito mopanda chilolezo. Mu kalata yomwe wasainira ndi wachiwiri kwa mkulu wayang'anira… ...
Asilikali a dziko lino atenga nawo gawo populumutsa anthu pafupipafupi 200 omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira ku Dwangwa m'boma la Nkhotakota. Malingana ndi lipoti lochokera ku khonsolo la Nkhotakota, asilikaliwa akugwiritsa ntchito mabwato awo apa… ...