Mvula Malawi
Alimi okhala ku Mpemba mu mzinda wa Blantyre, ali mkati mobzala mbeu nzawo kutsatira Mvula ya mphamvu yomwe inagwa m'derali mu usiku wa pa 9 November, 2023. Bambo silika ochokera m’mudzi mwa Mkoma m'dera la… ...