Twenty-year-old Busisiwe Lindani attracted the attention of those that attended the 2024 graduation at the Great Hall in Zomba as…
M’modzi mwa anthu oyimba mdziko muno Shammah Vocals wapempha mipingo kuti ikhale patsogolo yochititsa misonkhano ya achinyamata kuti idziwalimbikitsa zatsogolo…
Everlasting Life Missionary Church says it is its wish to reach out to the youths with words of God apart…
Hilton Banda, Managing Director of a mining exploration and consultancy company Akatswiri Holdings, on Sunday handed over an eight seater…
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Joyce Banda, apempha boma ndi mabungwe omwe akugawa chimanga kwa anthu omwe akhudzidwa ndi…
Catholic Development Commission in Malawi (CADECOM) in the Zomba Diocese has introduced a project called Food Crisis Response which will…
Chipatala cha mpingo wakatolika cha Pirimiti mu Boma la Zomba achitseka potsatira kusamvetsetsana komwe kulipo pakati pa ogwira ntchito ndi…
Member of Parliament for Zomba Central Bester Awali on Monday told Parliament that Agricultural Commercialisation (AGCOM) project which government is…
Mfumu Makungula a mdera la T/A Nkagula Boma la Zomba akuyimba lokoma pakhomo pawo chifukwa akupha makwacha ndi ng'ombe za…
Yemwe akufuna kudzayimira chipani cha Democratic Progressive m'dera la Zomba Thondwe pachisankho chakunyumba yamalamulo mi chaka cha 2025 a Dumisani…
Bungwe la Southern Region Water Board (SRWB) yati ili ndi chikonzero chomanga dam lalikulu ku Domasi m'boma la Zomba limene…
A 22-year-old young innovator, Stuart Nankhumwa, has made a device capable of tracking vehicles which he says will make it…
Advancing Girls Education in Africa (Age Africa) has donated assorted items to 10 girls at Masongola Secondary School in Zomba…
Bwalo la milandu ku Zomba lapeza olakwa bambo wina Chimwemwe Zololo yemwe amafuna kugulitsa mwana omupeza kwa bambo wina ochita…
Mkumano wa nambala 19 wama Khansala komanso wa Phungu yekhayo wamu mzinda wa Zomba omwe pachingerezi umatchedwa Full Council walephereka…