Namondwe Gezani adzetsa nyengo ya mvula ya mphamvu ku Malawi
Pamene Namondwe otchedwa Gezani adakang’antha dziko la Madagascar masiku apitawa, Nthambi yoona za nyengo mdziko muno ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati ku Malawi kuno m’maola 24-36 akudzawa kukhale nyengo ya… ...