Likakuona litsilo siikata: Mutharika alepheretsa msonkhano wa Chakwera
Patatha sabata mvula italepheretsa mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha Malawi Congress (MCP) a Lazarus Chakwera kuyankhula kwa owatsatira, a Chakwera akakamizidwa kupangitsa msonkhano wawo lamulungu mmalo mwa la loweruka. Izi zadza khonsolo ya m'boma… ...