Wakhwidzingiwa kamba kopezeka ndi wayilesi zakanema
Apolisi ku Kasungu akusunga mchitokosi njonda ina ya zaka 35 zakubadwa kamba kopezeka ndi katundu monga wayilesi za kanema zinayi za mtundu wa plasma ndipo njondayi ikuganiziridwa kuti idachita mokuba katunduyi. Wachiwiri kwa mneneli wa… ...