Mpira wa miyendo wa atsikana ukuyenda bwino – Migogo
Mtsogoleri wa bungwe la National Women's Football a Adelaide Migogo wati mphoto imodzi yomwe Malawi yapeza yomwe wawina Leticia Chinyamula kukhala osewela yemwe adzakhale wapamwamba mtsogolomu zawonetsa kuti osewerawa ali ndi kuthekera kochita bwino kwambiri… ...