Matenda a mphere avuta ku Dedza
Akuluakulu a ofesi ya zaumoyo ku khonsolo ya m'boma la Dedza atsimikiza kuti madera a m'bomali mwabuka matenda a zilonda zapakhungu omwe ndi kuphatikizapo mphere zomwe ati zagwira anthu ochulukirapo. Malingana ndi ofalitsa nkhani ku… ...