Kalindo akuchititsa zionetsero ku Zomba
Mtsogoleri wa Malawi First Bon Kalindo ali mu mzinda wa Zomba kuchita ziwonetsero zosakondwa ndi kugwa kwa mphamvu ya kwacha, kukwera kwa mitengo ya zinthu komanso kuchepa kwa malipiro anthu ogwira ntchito Boma. Ziwonetserozi zayambira… ...