![Malawi Protests leader Bon Kalindo has been arrested on several occassions since he started leading demonstrations against the Lazarus Chakwera administration](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/12/Bon-Kalindo-2-235x176.webp)
A Kalindo akhalabe mkambolimboli uku akudikira chigamulo
A Bon Kalindo akhala akusungidwabe mchitokosi cha apolisi uku akudikira chigamulo kuchokera kwa woweruza milandu a Muhammad Maxwell Chande lachisanu likudzali pa 15 December. A Kalindo anawanjata sabata latha m'boma la Zomba powaganizira kuti iwo… ...